Chorus (revolver)
Its a bagi party
Cheka chibukucho tiyake
Utha kubwela usanadye
Chifukwa its a bagi party
Verse 1 (stich fray)
Bring no bottle
Mkunda, gin, wine kwanu konko
Wachoka osadya uzidya mom'mo
Mom'mo mom'mo mom'mo mom'mo
Uzidya mom'mo mom'mo mom'mo mom'mo YEAH YEAH
Tili kuno sitichoka
Awuzeni amayiwo ubwele wokha wokha
Wadzulo wadzana chifukwa sitivokha
Tinabadwa nazo izi sizapompa YEAH
Tili kuno sitichoka
Awuzeni amayiwo ubwele wokha wokha
Wadzulo wadzana chifukwa sitivokha
Tinabadwa nazo izi sizapompa YEAH EH
(AHHH IWE) mundibudulira
Mundibudulira, bwino bwino, bwino mundibudulira
(AHHH IWE) mundibudulira
Mundibudulira, vina bwino iwe undibudulira
(chorus)
Verse 2 (judagaga)
Its a friday night, fans ikulowa out
Green, special, stout, koma zoti ndivaya i doubt
Am at my joint ku nancholi
Fans imanditcha ka duli
Bagi ndi number one
Anganditsuse ndani
Ena atathima thi, ndimangofila dim
Ena akumwa zowawa ngati akumwa mandimu
2 mina ablakilatu
Escom yathekelatu
Thats when we start to party, call it the bagi party
Vina osangoyima like a statue of liberty
Thats when we start to party, call it a bagi party
Thats when we start to party, call it a bagi party
Thats when we start to party, call it a bagi party
(chorus)
Verse 3(revolver)
Chapa den undipeze, tingosisa zi masese
Muwuzeni mkazi wanga ngati wakwiya nazo athese
Packet, no bottle
Mabebi, no photo
Tiyake tivokhe
Tivine titote-le
Gwila chibele bele bele belemuda
Ponya chimwendo, lero sitichoka mpaka kucha
Gwila chibele chibele bele belemuda
Ponya chimwendo, lero sitichoka mpaka kucha
Back to the drinking, ka bawa kumutu kayamba kuchepela
Looking like tikumenya bwalo likule chifukwa tikumenya cirlular
Sip, pass sip, pass tiki-taka
Tingoyamba kufinyila tikachedwa kuyaka
Artist: Love And Rockets
Artist: Kylie Minogue